Mateyu 19:7 - Buku Lopatulika7 Iwo ananena kwa Iye, Nanga chifukwa ninji Mose analamula kupatsa kalata yachilekaniro, ndi kumchotsa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Iwo ananena kwa Iye, Nanga chifukwa ninji Mose analamula kupatsa kalata wa chilekaniro, ndi kumchotsa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Afarisi aja adamufunsa kuti, “Nanga bwanji Mose adalamula kuti mwamuna azipatsa mkazi wake kalata ya chisudzulo kenaka nkumuchotsa?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndipo iwo anamufunsa nati, “Nanga nʼchifukwa chiyani Mose analamula kuti mwamuna azipatsa mkazi wake kalata ya chisudzulo ndi kumuchotsa?” Onani mutuwo |