Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 19:25 - Buku Lopatulika

25 Ndipo ophunzira, pamene anamva, anazizwa kwambiri, nanena, Ngati nkutero angapulumuke ndani?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndipo ophunzira, pamene anamva, anazizwa kwambiri, nanena, Ngati nkutero angapulumuke ndani?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Pamene ophunzira aja adamva zimenezi, adadabwa kwambiri nati, “Tsono nanga angathe kupulumuka ndani?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Ophunzira atamva zimenezi, anadabwa kwambiri ndipo anamufunsa kuti, “Nanga angapulumuke ndani?”

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 19:25
7 Mawu Ofanana  

Ndiponso ndinena kwa inu, Nkwapafupi kuti ngamira ipyole diso la singano, koposa mwini chuma kulowa Ufumu wa Kumwamba.


Ndipo Yesu anawayang'ana, nati kwa iwo, Ichi sichitheka ndi anthu, koma zinthu zonse zitheka ndi Mulungu.


Ndipo akadaleka kufupikitsidwa masiku awo, sakadapulumuka munthu aliyense: koma chifukwa cha osankhidwawo masiku awo adzafupikitsidwa.


Ndipo Ambuye akadapanda kufupikitsa masikuwo, sakadapulumuka munthu mmodzi yense; koma chifukwa cha osankhidwa amene anawasankha, anafupikitsa masikuwo.


pakuti, aliyense amene adzaitana pa dzina la Ambuye adzapulumuka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa