Mateyu 19:13 - Buku Lopatulika13 Pamenepo anadza nato tiana kwa Iye, kuti Iye aike manja ake pa ito, ndi kupemphera: koma ophunzirawo anawadzudzula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pamenepo anadza nato tiana kwa Iye, kuti Iye aike manja ake pa ito, ndi kupemphera: koma ophunzirawo anawadzudzula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Anthu ena ankabwera ndi ana kuti Yesu aŵasanjike manja ndi kuŵapempherera, ophunzira ake nkumaŵazazira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pamenepo anabwera nawo ana kwa Yesu kuti awasanjike manja ndi kuwapempherera. Koma ophunzira ake anadzudzula amene anabweretsa anawo. Onani mutuwo |