Mateyu 18:1 - Buku Lopatulika1 Nthawi yomweyo ophunzira anadza kwa Yesu, nanena, Ndani kodi ali wopambana mu Ufumu wa Kumwamba? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Nthawi yomweyo ophunzira anadza kwa Yesu, nanena, Ndani kodi ali wopambana mu Ufumu wa Kumwamba? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Nthaŵi yomweyo ophunzira aja adadzamufunsa Yesu kuti, “Kodi mu Ufumu wakumwamba wamkulu koposa onse ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pa nthawi imeneyo ophunzira anabwera kwa Yesu ndipo anamufunsa kuti, “Wamkulu woposa onse ndani mu ufumu wakumwamba?” Onani mutuwo |