Mateyu 18:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo pamene Yesu anaitana kamwana, anakaimitsa pakati pao, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo pamene Yesu anaitana kamwana, anakaimitsa pakati pao, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Apo Yesu adaitana mwana namuimiritsa pakati pao, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anayitana kamwana kakangʼono ndi kukayimiritsa pakati pawo. Onani mutuwo |