Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 17:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo iwo, pokweza maso ao sanaone munthu, koma Yesu yekha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo iwo, pokweza maso ao sanaone munthu, koma Yesu yekha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Iwo aja poŵeramuka, adangoona kuti palibe munthu winanso, koma Yesu yekha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Atayangʼana, sanaone wina aliyense kupatula Yesu yekha.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 17:8
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Yesu anadza, nawakhudza nati, Ukani, musaopa.


Ndipo pamene anali kutsika paphiri, Yesu anawalamula iwo kuti, Musakauze munthu choonekacho, kufikira Mwana wa Munthu adadzauka kwa akufa.


Ndipo dzidzidzi pounguzaunguza, sanapenye munthu wina yense, koma Yesu yekha, ndi iwo eni.


Ndipo pakutero mauwo, Yesu anapezedwa ali yekha. Ndipo iwo anakhala chete, ndipo sanauze munthu aliyense masiku aja kanthu konse ka izo anaziona.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa