Mateyu 17:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo pamene iwo anadza kukhamu la anthu, kunafika kwa Iye munthu, namgwadira Iye, nati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo pamene iwo anadza kukhamu la anthu, kunafika kwa Iye munthu, namgwadira Iye, nati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pamene iwo adafikanso kumene kunali khamu la anthu kuja, munthu wina adadzagwadira Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Atafika ku gulu la anthu, munthu wina anamuyandikira Yesu ndi kugwada pamaso pake. Onani mutuwo |