Mateyu 17:13 - Buku Lopatulika13 Pomwepo ophunzira anazindikira kuti analankhula nao za Yohane Mbatizi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pomwepo ophunzira anazindikira kuti analankhula nao za Yohane Mbatizi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Pamenepo ophunzira aja adazindikira kuti ankaŵauza za Yohane Mbatizi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pamenepo ophunzira anazindikira kuti amawawuza za Yohane Mʼbatizi. Onani mutuwo |