Mateyu 15:7 - Buku Lopatulika7 Onyenga inu! Yesaya ananenera bwino za inu, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Onyenga inu! Yesaya ananenera bwino za inu, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Inu anthu achiphamaso, ndithu mneneri Yesaya adaanenadi zoona muja adaati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Inu anthu achiphamaso, Yesaya ananenera za inu kuti, Onani mutuwo |