Mateyu 15:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo m'mene Iye anauza makamuwo amuke, analowa m'ngalawa, nafika m'malire a Magadani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo m'mene Iye anauza makamuwo amuke, analowa m'ngalawa, nafika m'malire a Magadani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Pambuyo pake Yesu adatsazikana nawo anthu aja, kenaka Iye adaloŵa m'chombo napita ku dera la Magadani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Yesu atatha kuwuza gululo kuti lipite kwawo, analowa mʼbwato ndipo anapita kudera la Magadala. Onani mutuwo |