Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mateyu 15:38 - Buku Lopatulika

38 Ndipo anadyawo anali amuna zikwi zinai kuwaleka akazi ndi ana.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

38 Ndipo anadyawo anali amuna zikwi zinai kuwaleka akazi ndi ana.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

38 Koma tsono anthu amene adaadyawo, analipo zikwi zinai amuna okha, osaŵerenga akazi ndi ana.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

38 Chiwerengero cha anthu amene anadya chinali 4,000 kupatula amayi ndi ana.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 15:38
2 Mawu Ofanana  

Ndipo onsewa anadya, nakhuta: ndipo anatola makombo otsala madengu asanu ndi awiri odzala.


Ndipo m'mene Iye anauza makamuwo amuke, analowa m'ngalawa, nafika m'malire a Magadani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa