Mateyu 15:2 - Buku Lopatulika2 Ophunzira anu alumphiranji miyambo ya makolo? Pakuti sasamba manja pakudya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ophunzira anu alumphiranji miyambo ya makolo? Pakuti sasamba manja pakudya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Chifukwa chiyani ophunzira anu sasunga mwambo wa makolo? Sasamba m'manja moyenera akamadya chakudya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Chifukwa chiyani ophunzira anu amaphwanya mwambo wa akuluakulu? Iwo sasamba mʼmanja pakudya!” Onani mutuwo |