Mateyu 15:1 - Buku Lopatulika1 Pomwepo anadza kwa Yesu Afarisi ndi alembi, ochokera ku Yerusalemu, nati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pomwepo anadza kwa Yesu Afarisi ndi alembi, ochokera ku Yerusalemu, nati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku lina Afarisi ena ndi aphunzitsi ena a Malamulo adadza kwa Yesu kuchokera ku Yerusalemu. Adamufunsa kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pamenepo Afarisi ena ndi aphunzitsi amalamulo anabwera kwa Yesu kuchokera ku Yerusalemu ndipo anamufunsa kuti, Onani mutuwo |