Mateyu 14:36 - Buku Lopatulika36 ndipo anampempha Iye, kuti akhudze mphonje yokha ya chovala chake; ndipo onse amene anamkhudza anachiritsidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 ndipo anampempha Iye, kuti akhudze yokha mphonje ya chovala chake; ndipo onse amene anamkhudza anachiritsidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Adampempha kuti aŵalole odwalawo kungokhudza ngakhale mphonje ya chovala chake. Mwakuti onse amene ankaikhudza, ankachira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Ndipo anamupempha alole kuti akhudze mphonje ya mkanjo wake, ndipo onse amene anamukhudza anachiritsidwa. Onani mutuwo |