Mateyu 15:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Iye anayankha, nati kwa iwo, Inunso mulumphiranji lamulo la Mulungu chifukwa cha miyambo yanu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Iye anayankha, nati kwa iwo, Inunso mulumphiranji lamulo la Mulungu chifukwa cha miyambo yanu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Yesu adaŵayankha kuti, “Nanga bwanji inuyo, chifukwa choumirira miyambo yanu, mumaphwanya lamulo la Mulungu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Yesu anayankha kuti, “Nanga chifukwa chiyani inu mumaphwanya lamulo la Mulungu chifukwa cha mwambo wa makolo anu? Onani mutuwo |