Mateyu 15:18 - Buku Lopatulika18 Koma zakutuluka m'kamwa zichokera mumtima; ndizo ziipitsa munthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Koma zakutuluka m'kamwa zichokera mumtima; ndizo ziipitsa munthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Koma zotuluka m'kamwa mwa munthu zimachokera mu mtima, ndipo zimenezi ndizo zimamuipitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Koma zinthu zimene zituluka mʼkamwa zimachokera mu mtima ndipo zimenezi zimamuchititsa munthu kukhala woyipa. Onani mutuwo |