Mateyu 15:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Petro anayankha nati kwa Iye, Mutifotokozere ife fanizoli. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Petro anayankha nati kwa Iye, Mutifotokozere ife fanizoli. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Apo Petro adampempha kuti, “Timasulirenitu fanizoli.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Petro anati, “Timasulireni fanizoli.” Onani mutuwo |