Mateyu 15:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Iye anati, Kodi inunso mukhala chipulukirire? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Iye anati, Kodi inunso mukhala chipulukirire? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Yesu adati, “Kani ngakhale inunso simumvetsa? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Yesu anawafunsa kuti, “Kani ngakhale inunso simumvetsa? Onani mutuwo |