Mateyu 15:12 - Buku Lopatulika12 Pomwepo anadza ophunzira, nanena kwa Iye, Mudziwa kodi kuti Afarisi anakhumudwa pakumva chonenacho? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pomwepo anadza ophunzira, nanena kwa Iye, Mudziwa kodi kuti Afarisi anakhumudwa pakumva chonenacho? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pamenepo ophunzira ake adadzamufunsa kuti, “Kodi mukudziŵa kuti Afarisi aja akhumudwa atamva zija mwanenazi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pamenepo ophunzira anabwera kwa Iye ndipo anamufunsa kuti, “Kodi mukudziwa kuti Afarisi anakhumudwa pamene anamva mawu aja?” Onani mutuwo |