Mateyu 15:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Iye anaitana makamuwo nati kwa iwo, Imvani, nimudziwitse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Iye anaitana makamuwo nati kwa iwo, Imvani, nimudziwitse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pambuyo pake Yesu adaitana anthu aja kuti adze pafupi, ndipo adaŵauza kuti, “Mverani ndipo mumvetse bwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yesu anayitana gulu la anthu nati, “Mverani ndipo zindikirani. Onani mutuwo |