Mateyu 14:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti Yohane ananena kwa iye, Sikuloledwa kwa iwe kukhala naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti Yohane ananena kwa iye, Sikuloledwa kwa iwe kukhala naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pakuti Yohane adaauza Herode kuti, “Nkulakwira Malamulo kumukwatira mkaziyo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Chifukwa Yohane anakhala akunena kwa iye kuti, “Sichololedwa kwa inu kutenga mkaziyo.” Onani mutuwo |