Mateyu 14:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo pamene iwo anaoloka, anafika kumtunda, ku Genesarete. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo pamene iwo anaoloka, anafika kumtunda, ku Genesarete. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Tsono onse adaoloka nyanja nakafika ku Genesarete. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Atawoloka, anafika ku Genesareti. Onani mutuwo |