Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 14:26 - Buku Lopatulika

26 Koma m'mene ophunzirawo anamuona Iye, alikuyenda pamadzi, ananthunthumira, nati, Ndi mzukwa! Ndipo anafuula ndi mantha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Koma m'mene ophunzirawo anamuona Iye, alikuyenda pamadzi, ananthunthumira, nati, Ndi mzukwa! Ndipo anafuula ndi mantha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Pamene ophunzira aja adamuwona akuyenda pa madzi, adaopsedwa nati, “Ndi mzukwa!” Ndipo adayamba kukuwa chifukwa cha mantha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Ophunzira atamuona akuyenda pa nyanja, anaopa nati, “Ndi mzukwa!” Ndipo analira chifukwa cha mantha.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 14:26
11 Mawu Ofanana  

ndipo m'mene sanapeze mtembo wake, anadza, nanena kuti adaona m'masomphenya angelo, amene ananena kuti ali ndi moyo Iye.


Koma anaopsedwa ndi kuchita mantha, nayesa alikuona mzimu.


Ndipo anawatsegulira mitima yao, kuti adziwitse malembo;


ndipo m'mene anakhala ndi mantha naweramira pansi nkhope zao, anati kwa iwo, Mufuniranji wamoyo pa akufa?


Koma anati kwa iye, Wamisala iwe. Ndipo analimbika ndi kunena kuti nkutero. Ndipo ananena, Ndiye mngelo wake.


Ndipo pamene ndinamuona Iye, ndinagwa pa mapazi ake ngati wakufa; ndipo anaika dzanja lake lamanja pa ine, nati, Usaope, Ine ndine Woyamba ndi Wotsiriza,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa