Mateyu 14:24 - Buku Lopatulika24 Koma pomwepo ngalawa idafika pakati pa nyanja, yozunzika ndi mafunde; pakuti mphepo inadza mokomana nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Koma pomwepo ngalawa idafika pakati pa nyanja, yozunzika ndi mafunde; pakuti mphepo inadza mokomana nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Pamenepo nkuti chombo chija chili kutalitali ndi mtunda, chikuvutika ndi mafunde, chifukwa chinali chitayang'anana ndi mphepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Pamenepo nʼkuti bwato litapita patali pangʼono kuchokera ku mtunda ndipo linavutika ndi mafunde chifukwa mphepo inkawomba mokumana nalo. Onani mutuwo |