Mateyu 14:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anadyawo anali amuna monga zikwi zisanu, kuwaleka akazi ndi ana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anadyawo anali amuna monga zikwi zisanu, kuwaleka akazi ndi ana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma tsono anthu amene adaadyawo analipo ngati zikwi zisanu amuna okha, osaŵerenga akazi ndi ana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Chiwerengero cha amene anadya kupatulako amayi ndi ana chinali pafupifupi amuna 5,000. Onani mutuwo |