Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 14:22 - Buku Lopatulika

22 Ndipo pomwepo Iye anafulumiza ophunzira alowe m'ngalawa, ndi kumtsogolera Iye kutsidya lija, kufikira Iye atauza makamu amuke.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo pomwepo Iye anafulumiza ophunzira alowe m'ngalawa, ndi kumtsogolera Iye kutsidya lija, kufikira Iye atauza makamu amuke.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Madzulo omwewo Yesu adalamula ophunzira ake kuti aloŵe m'chombo, atsogole kupita ku tsidya, pamene Iye akuuza anthu kuti azipita kwao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Nthawi yomweyo anawawuza ophunzira ake kuti alowe mʼbwato ndi kuti atsogole kupita kutsidya lina pamene Iye ankawuza anthu kuti azipita kwawo.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 14:22
6 Mawu Ofanana  

Pomwepo Iye anasiya makamuwo, nalowa m'nyumba; ndimo ophunzira ake anadza kwa Iye, nanena, Mutitanthauzire fanizo lija la namsongole wa m'munda.


Ndipo anadyawo anali amuna monga zikwi zisanu, kuwaleka akazi ndi ana.


Ndipo m'mene Iye anauza makamuwo amuke, analowa m'ngalawa, nafika m'malire a Magadani.


Koma pamene Silasi ndi Timoteo anadza potsika ku Masedoniya, Paulo anapsinjidwa ndi mau, nachitira umboni kwa Ayuda kuti Yesu ndiye Khristu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa