Mateyu 14:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Iye anati, Mudze nazo kuno kwa Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Iye anati, Mudze nazo kuno kwa Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Yesu adati, “Bwera nazoni kuno.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Koma Iye anati, “Bweretsani kwa Ine.” Onani mutuwo |