Mateyu 14:17 - Buku Lopatulika17 Koma iwo ananena kwa Iye, Ife tilibe kanthu pano koma mikate isanu, ndi nsomba ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Koma iwo ananena kwa Iye, Ife tilibe kanthu pano koma mikate isanu, ndi nsomba ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Iwo adati, “Pano tili ndi buledi msanu yekha ndi nsomba ziŵiri, basi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Iwo anayankha kuti, “Tili ndi malofu asanu okha a buledi ndi nsomba ziwiri.” Onani mutuwo |