Mateyu 14:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Yesu pakumva, anachokera kumeneko m'ngalawa, kunka kumalo achipululu pa yekha; ndipo makamu, pamene anamva, anamtsata Iye mumtunda kuchokera m'midzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Yesu pakumva, anachokera kumeneko m'ngalawa, kunka kumalo achipululu pa yekha; ndipo makamu, pamene anamva, anamtsata Iye mumtunda kuchokera m'midzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Yesu atazimva zimenezi, adachokako kumeneko m'chombo, kuti apite kwayekha kwazii. Koma anthu atamva, adayenda pa mtunda namlondola kuchokera ku mizinda yao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Yesu atamva zimene zinachitika, anachoka pa bwato mwachinsinsi kupita kumalo a yekha. Magulu a anthu atamva izi anamutsatira Iye poyenda pansi kuchokera ku mizinda. Onani mutuwo |