Mateyu 14:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo ophunzira ake anadza, natola mtembo, nauika; ndipo anadza nauza Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo ophunzira ake anadza, natola mtembo, nauika; ndipo anadza nauza Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pambuyo pake ophunzira a Yohane adabwera nadzatenga mtembo wake nkukauika m'manda. Kenaka adapita kukauza Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ophunzira a Yohane anabwera nadzatenga mtembo wake ndi kukawuyika mʼmanda. Pomwepo iwo anapita kukamuwuza Yesu. Onani mutuwo |