Mateyu 13:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo m'mene dzuwa linakwera zinapserera; ndipo popeza zinalibe mizu zinafota. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 ndipo popeza zinalibe mizu zinafota. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma pamene dzuŵa lidakwera, zidapserera kenaka zidauma, chifukwa zinali zosazika mizu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma dzuwa litakwera, mbewu zinapserera ndipo zinawuma chifukwa zinalibe mizu. Onani mutuwo |