Mateyu 13:7 - Buku Lopatulika7 Koma zina zinagwa paminga, ndipo mingayo inayanga, nkuzitsamwitsa izo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Koma zina zinagwa paminga, ndipo mingayo inayanga, nizitsamwitsa izo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mbeu zina zidagwera pa zitsamba zaminga. Zitsambazo pokula zidalanda chakudya cha mbeu zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mbewu zina zinagwa pa minga ndipo mingayo inayanga ndi kuzirepheretsa kukula. Onani mutuwo |