Mateyu 13:56 - Buku Lopatulika56 Ndipo alongo ake sali ndife onsewa? Ndipo Iyeyo adazitenga zinthu zonsezi kuti? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201456 Ndipo alongo ake sali ndife onsewa? Ndipo Iyeyo adazitenga zinthu zonsezi kuti? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa56 Kodi suja alongo ake onse ali nafe pompano? Nanga tsono zonsezi adazitenga kuti?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero56 Kodi alongo ake onse sali ndi ife? Tsono ndi kuti kumene anazitenga zinthu izi?” Onani mutuwo |