Mateyu 13:48 - Buku Lopatulika48 limene podzala, analivuulira pamtunda; ndipo m'mene anakhala pansi, anazisonkhanitsa zabwino m'zotengera, koma zoipa anazitaya kuthengo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 limene podzala, analivuulira pamtunda; ndipo m'mene anakhala pansi, anazisonkhanitsa zabwino m'zotengera, koma zoipa anazitaya kuthengo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Likadzaza, anthu amalikokera ku mtunda. Tsono amakhala pansi, nsomba zabwino nkumaziika m'madengu, zachabe nkumangozitaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Litadzaza, asodzi analikokera ku mtunda. Pomwepo anakhala pansi nasonkhanitsa nsomba zabwino mʼmadengu koma zoyipa anazitaya. Onani mutuwo |