Mateyu 13:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo makamu ambiri a anthu anasonkhanira kwa Iye, kotero kuti Iye analowa m'ngalawa, nakhala pansi, ndipo khamu lonse linaima pamtunda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo makamu ambiri a anthu anasonkhanira kwa Iye, kotero kuti Iye analowa m'ngalawa, nakhala pansi, ndipo khamu lonse linaima pamtunda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Anthu ambirimbiri adasonkhana kumene kunali Iye. Tsono Yesu adaloŵa m'chombo nakhala pansi, anthu onse aja ataima pa mtunda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Magulu a anthu anasonkhana mozungulira ndipo Iye analowa mʼbwato nakhala pansi ndipo anthu onse anayimirira ku mtunda. Onani mutuwo |