Mateyu 13:1 - Buku Lopatulika1 Tsiku lomwelo Yesu anatuluka m'nyumbamo, nakhala pansi m'mbali mwa nyanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Tsiku lomwelo Yesu anatuluka m'nyumbamo, nakhala pansi m'mbali mwa nyanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku lomwelo Yesu adatuluka m'nyumba nakakhala pansi m'mbali mwa nyanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsiku lomwelo Yesu anatuluka mʼnyumba ndipo anakhala mʼmbali mwa nyanja. Onani mutuwo |