Mateyu 13:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo ophunzirawo anadza, nati kwa Iye, Chifukwa chanji muphiphiritsira iwo m'mafanizo? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo ophunzirawo anadza, nati kwa Iye, Chifukwa chanji muphiphiritsira iwo m'mafanizo? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pambuyo pake ophunzira a Yesu aja adadzamufunsa kuti, “Kodi bwanji anthuŵa mumalankhula nawo m'mafanizo?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ophunzira anabwera kwa Iye ndikumufunsa kuti, “Chifukwa chiyani Inu mukuyankhula kwa anthu mʼmafanizo?” Onani mutuwo |