Mateyu 12:3 - Buku Lopatulika3 Koma Iye anati kwa iwo, Kodi simunawerenge chimene anachichita Davide, pamene anali ndi njala, ndi iwo amene anali naye? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Koma Iye anati kwa iwo, Kodi simunawerenga chimene anachichita Davide, pamene anali ndi njala, ndi iwo amene anali naye? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Iye adati, “Kani simudaŵerenge zimene adaachita Davide, pamene iye ndi anzake adaazingwa nayo njala? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iye anayankha kuti, “Kodi simunawerenge zimene anachita Davide pamene iye ndi anzake anamva njala? Onani mutuwo |