Mateyu 12:2 - Buku Lopatulika2 Koma Afarisi, pakuona, anati kwa Iye, Tapenyani, ophunzira anu achita chosaloleka tsiku la Sabata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma Afarisi, pakuona, anati kwa Iye, Tapenyani, ophunzira anu achita chosaloleka tsiku la Sabata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Pamene Afarisi adaona zimenezi, adauza Yesu kuti, “Taonani, ophunzira anu akuchita zimene siziloledwa pa tsiku la Sabata.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Afarisi ataona zimenezi anati kwa Iye, “Taonani! Ophunzira anu akuchita zosaloledwa pa tsiku la Sabata.” Onani mutuwo |