Mateyu 12:13 - Buku Lopatulika13 Pomwepo ananena Iye kwa munthuyo, Tansa dzanja lako. Ndipo iye analitansa, ndipo linabwezedwa lamoyo longa linzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pomwepo ananena Iye kwa munthuyo, Tansa dzanja lako. Ndipo iye analitansa, ndipo linabwezedwa lamoyo longa linzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Atatero, adalamula munthu uja kuti, “Tambalitsa dzanja lako.” Iye adalitambalitsa, ndipo dzanja lakelo lidakhalanso bwino ngati linzake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pamenepo Yesu anati kwa munthuyo, “Wongola dzanja lako.” Iye analiwongola ndipo linakhala monga linalili kale. Onani mutuwo |