Mateyu 12:12 - Buku Lopatulika12 Nanga kuposa kwake kwa munthu ndi nkhosa nkotani! Chifukwa cha ichi nkuloleka kuchita zabwino tsiku la Sabata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Nanga kuposa kwake kwa munthu ndi nkhosa nkotani! Chifukwa cha ichi nkuloleka kuchita zabwino tsiku la Sabata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Nanji munthu, amene amaposa nkhosa kutalitali! Ndiye kutitu Malamulo amalola kuchita zabwino pa tsiku la Sabata.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Nanga munthu sali oposa nkhosa kwambiri! Chifukwa chake nʼkololedwa kuchita zabwino pa Sabata.” Onani mutuwo |