Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 11:9 - Buku Lopatulika

9 Koma munatulukiranji? Kukaona mneneri kodi? Indetu, ndinena kwa inu, wakuposa mneneri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Koma munatulukiranji? Kukaona mneneri kodi? Indetu, ndinena kwa inu, wakuposa mneneri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Tanenanitu, mudaati mukaona chiyani? Mneneri kodi? Zoonadi, ndipo ndikunenetsa kuti mudakaona woposa mneneri amene.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Nanga munkapita kukaona chiyani? Mneneri kodi? Inde ndikuwuzani kuti munkakaona woposa mneneri.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 11:9
9 Mawu Ofanana  

Koma munatuluka kukaona chiyani? Munthu wovala zofewa kodi? Onani, akuvala zofewa ali m'nyumba zamafumu.


Ndipo pofuna kumupha iye, anaopa khamu la anthu, popeza anamuyesa iye mneneri.


Eya, ndipo iwetu kamwanawe, udzanenedwa mneneri wa Wamkulukulu; pakuti udzatsogolera Ambuye, kukonza njira zake.


Ndiponso, tikanena, Uchokera kwa anthu; anthu onse adzatiponya miyala: pakuti akopeka mtima, kuti Yohane ali mneneri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa