Mateyu 11:8 - Buku Lopatulika8 Koma munatuluka kukaona chiyani? Munthu wovala zofewa kodi? Onani, akuvala zofewa ali m'nyumba zamafumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma munatuluka kukaona chiyani? Munthu wovala zofewa kodi? Onani, akuvala zofewa ali m'nyumba zamafumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Nanga mudaati mukaona chiyani? Munthu wovala zofeŵa kodi? Iyai, anthu ovala zofeŵa amakhala m'nyumba za mafumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Nanga munkapita kukaona chiyani, munthu wovala zokongola? Ayi, wovala zokongola amakhala mʼnyumba za mafumu. Onani mutuwo |