Mateyu 11:16 - Buku Lopatulika16 Koma ndidzafanizira ndi chiyani obadwa awa a makono? Ali ofanana ndi ana akukhala m'mabwalo a malonda, amene alikuitana anzao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma ndidzafanizira ndi chiyani obadwa awa a makono? Ali ofanana ndi ana akukhala m'mabwalo a malonda, amene alikuitana anzao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 “Kaya anthu amakonoŵa ndingaŵafanizire ndi chiyani? Ali ngati ana okangana pa msika, ena akufunsa anzao kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “Kodi mʼbado uwu ndingawufanizire ndi chiyani? Uli ngati ana opezeka mʼmisika amene akuyitana anzawo nʼkumati: Onani mutuwo |