Mateyu 10:9 - Buku Lopatulika9 Musadzitengere ndalama zagolide, kapena zasiliva, kapena zakobiri m'malamba mwanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Musadzitengere ndalama zagolide, kapena zasiliva, kapena zakobiri m'malamba mwanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Musatenge ndalama m'zikwama, kaya nzagolide, kaya nzasiliva, kaya nzakopala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Musatenge ndalama zagolide kapena zasiliva kapena zakopala mʼzikwama mwanu; Onani mutuwo |