Mateyu 10:6 - Buku Lopatulika6 koma makamaka mupite kunkhosa zosokera za banja la Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 koma makamaka mupite kunkhosa zosokera za banja la Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma makamaka mupite kwa Aisraele amene ali ngati nkhosa zotayika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma pitani kwa nkhosa zotayika za banja la Israeli. Onani mutuwo |