Mateyu 10:39 - Buku Lopatulika39 Iye amene apeza moyo wake, adzautaya; ndi iye amene ataya moyo wake, chifukwa cha Ine, adzaupeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Iye amene apeza moyo wake, adzautaya; ndi iye amene ataya moyo wake, chifukwa cha Ine, adzaupeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Munthu woyesa kusunga moyo wake, adzautaya, ndipo wotaya moyo wake chifukwa cha Ine, adzausunga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Aliyense amene asunga moyo wake adzawutaya koma aliyense amene ataya moyo chifukwa cha Ine adzawupeza. Onani mutuwo |