Mateyu 10:32 - Buku Lopatulika32 Chifukwa chake yense amene adzavomereza Ine pamaso pa anthu, Inenso ndidzamvomereza iye pamaso pa Atate wanga wa Kumwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Chifukwa chake yense amene adzavomereza Ine pamaso pa anthu, Inenso ndidzamvomereza iye pamaso pa Atate wanga wa Kumwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 “Aliyense wondivomereza pamaso pa anthu, Inenso ndidzamuvomereza pamaso pa Atate anga amene ali Kumwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 “Aliyense amene avomereza Ine pamaso pa anthu, Inenso ndidzavomereza pamaso pa Atate anga akumwamba. Onani mutuwo |