Mateyu 10:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo polowa m'nyumba muwalonjere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo polowa m'nyumba muwalonjere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Poloŵa m'nyumba, muzikanena kuti, ‘Mtendere ukhale ndi inu’. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pamene mulowa mʼnyumba mupereke moni. Onani mutuwo |