Mateyu 10:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo m'mzinda uliwonse, kapena m'mudzi, mukalowamo, mufunsitse amene ali woyenera momwemo; ndipo bakhalani komweko kufikira mutulukamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo m'mzinda uliwonse, kapena m'mudzi. Mukalowamo, mufunsitse amene ali woyenera momwemo; ndipo bakhalani komweko kufikira mutulukamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 “Pamene mwaloŵa mu mzinda kapena m'mudzi uliwonse, mufunsitse za munthu wofunadi kukulandirani. Mukakhale kunyumba kwake mpaka nthaŵi yochoka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mukalowa mu mzinda ndi mʼmudzi uliwonse, funafunani munthu woyenera ndipo mukhale mʼnyumba mwake kufikira mutachoka. Onani mutuwo |